Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 16:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo macitidwe ena a Omri anawacita, ndi mphamvu yace anaionetsa, kodi sizilembedwa m'buku la macitidwe a mafumu a Israyeli?

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 16

Onani 1 Mafumu 16:27 nkhani