Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 16:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kunali tsono, pakuona Zimri kuti nkhondo yalowa m'mudzi, anakwera pa nsanja ya nyumba ya mfumu, nadzitenthera ndi mota nyumba ya mfumu, nafa;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 16

Onani 1 Mafumu 16:18 nkhani