Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 16:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, atalowa ufumu wace, nakhala pa mpando wacifumu wace, anawakantha onse a m'nyumba ya Basa, osamsiyira mwana wamwamuna ndi mmodzi yense, kapena wa abale ace, kapena wa mabwenzi ace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 16

Onani 1 Mafumu 16:11 nkhani