Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 15:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsonokunacitika, pokhalamfumu iye, anakantha nyumba yonse ya Yerobiamu, osasiyako wamoyo ndi mmodzi yense wa Yerobiamu, kufikira adamuononga monga mwa mau a Yehova, amene analankhula pa dzanja la mtumiki wace Ahiya wa ku Silo;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 15

Onani 1 Mafumu 15:29 nkhani