Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 15:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Benihadadi anamvera mfumu Asa, natuma akazembe a nkhondo ace kukathira nkhondo ku midzi ya Israyeli, napasula Iyoni, ndi Dani, ndi AbeliBeti-Maaka, ndi Kineroti wonse, ndi dziko lonse la Nafitali.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 15

Onani 1 Mafumu 15:20 nkhani