Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 14:30-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Ndipo panali nkhondo pakati pa Rehabiamu ndi Yerobiamu masiku ao onse.

31. Nagona Rehabiamu ndi makolo ace, naikidwa kwa makolo ace m'mudzi wa Davide. Ndipo dzina la amace linali Naama M-amoni, nalowa ufumu m'malo mwace Abiya mwana wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 14