Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 14:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Nthawi yomweyo Abiya mwana wa Yerobiamu anadwala.

2. Ndipo Yerobiamu ananena ndi mkazi wace, Unyamuke, nudzizimbaitse, ungadziwike kuti ndiwe mkazi wa Yerobiamu, nupite ku Silo; taona, kumeneko kuli Ahiya mneneri uja anandiuza ine ndidzakhala mfumu ya anthu awa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 14