Popeza mau aja anawapfuula mwa mau a Yehova kutemberera guwa la nsembe la ku Beteli, ndi kutemberera nyumba zonse za misanje iri m'midzi ya ku Samariya, adzacitika ndithu.