Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 13:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mneneri amene uja anambweza panjirayo atamva, anati, Ndiye munthu uja wa Mulungu amene sanamvera mau a Yehova; cifukwa cace Yehova wampereka kwa mkango, numkadzula numupha, monga mwa mau a Yehova analankhula nayewo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13

Onani 1 Mafumu 13:26 nkhani