Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 13:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti mau a Yehova anadza kwa ine, nati Usakadye mkate, kapena kumwa madzi kumeneko, kapena kubwerera njira yomweyo unadzerayo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13

Onani 1 Mafumu 13:17 nkhani