Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 12:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mfumu Rehabiamu anatuma Adoramu wamsonkho, ndipo Aisrayeli onse anamponya miyala, nafa. Ndipo mfumu Rehabiamu anafulumira kulowa m'gareta wace kuthawira ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 12

Onani 1 Mafumu 12:18 nkhani