Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 11:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nditero popeza iwo anandisiya, napembedza Asitoreti mulungu wa Azidoni, ndi Kemosi mulungu wa Amoabu, ndi Milikomu mulungu wa ana a Amoni, osayenda m'njira zanga, kucita cimene ciyenera pamaso panga, ndi kusunga malemba anga ndi maweruzo anga, monga umo anatero Davide atate wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 11

Onani 1 Mafumu 11:33 nkhani