Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 10:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma sindinakhulupira mau amenewo mpaka ndafika ine kuno, ndaona ndi maso anga; ndipo taonani, anangondiuza dera lina lokha; nzeru zanu ndi zokoma zanu zakula pa mbiri ndinaimvayo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 10

Onani 1 Mafumu 10:7 nkhani