Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 10:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zikho zomwera zonse za mfumu Solomo zinali zagolidi, ndi zotengera zonse za nyumba yochedwa Nkhalango ya Lebano zinali zagolidi yekha yekha, panalibe zasiliva, pakuti siliva ana ngoyesedwa opanda pace masiku onse a Solomo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 10

Onani 1 Mafumu 10:21 nkhani