Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 10:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi malihawo mazana atatu a golidi wonsansantha, libawo limodzi linapangidwa ndi miyeso itatu ya golidi; ndipo mfumu inazisungira zonse m'nyumba yochedwa Nkhalango ya Lebano.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 10

Onani 1 Mafumu 10:17 nkhani