Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 1:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Zadoki wansembe ndi Natani mneneri akamdzoze kumeneko akhale mfumu ya Israyeli; ndipo muombe lipenga, ndi kuti, Mfumu Solomo akhale ndi moyo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:34 nkhani