Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 1:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu Davide anati, Kandiitanireni Zadoki wansembeyo, ndi Natani mneneriyo, ndi Benaya mwana wa Yehoyada. Iwo nalowa pamaso pa mfumu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:32 nkhani