Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono anafunafuna m'malire monse a Israyeli namwali wokongola, napeza Abisagi wa ku-Sunamu, nabwera naye kwa mfumu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:3 nkhani