Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 1:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono mfumu Davide anayankha, nati, Ndiitanireni Batiseba. Ndipo iye analowa pamaso pa mfumu, naima pamaso pa mfumu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:28 nkhani