Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 1:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Muka nulowe kwa mfumu Davide, nukati kwa iye, Mbuye wanga mfumu, kodi simunalumbirira mdzakazi wanu, ndi kuti, Zedi Solomo mwana wako adzakhala mfumu nditamuka ine, nadzakhala pa mpando wanga wadfumu? ndipo Adoniya akhaliranji mfumu?

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:13 nkhani