Koma anadzanso 7 Nikodemo, amene anadza kwa iye usiku poyamba paja, alikutenga cisanganizo ca mure ndi aloe, monga miyeso zana.