Luka 7:48-50 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndipo anati kwa mkazi, Macimo ako akhululukidwa. Ndipo Iyeanati kwa mkaziyo, Cikhulupiriro cako cakupulumutsa iwe