Popeza ife amene takhulupira tilowa mpumulowo, monga momwe ananena,Monga ndalumbira mu mkwiyowanga,Ngati adzalowa mpumulo wanga:zingakhale nebitozo zidatsirizika kuyambira kuzika kwa dziko lapansi.