Ndi monga copfunda mudzaipindaMonga maraya, ndipo idzasanduka;Koma Inu ndinu yemweyo,Ndipo zaka zanu sizidzatha.