20. ndiponso Ambuye azindikira zolingirira za mzeru, kuti ziri zopanda pace.
21. Cifukwa cace palibemmodzi adziamande mwa anthu. Pakuti zinthu onse nzanu;
22. ngati Paulo, kapena Apolo, kapena Kefa, kapena dziko apansi, kapena moyo, kapena imfa, capena za makono ano, kapena drinkudza; zonse ndi zanu;
23. kona inu ndinu a Kristu; ndi Kristu ndiye wa Mulungu.