20. mfumu ya ku Simironi-meroni, imodzi; mfumu ya ku Akasafu, imodzi;
21. mfumu ya ku Taanaki, imodzi; mfumu ya ku Megido, imodzi;
22. mfumu ya ku Kadesi, imodzi; mfumu ya ku Yokineamu ku Karimeli, imodzi;
23. mfumuya ku Doro, mpaka ponyamuka pa Doro, imodzi; mfumu ya ku Goimu m'Giligala, imodzi;
24. mfumu ya ku Tiriza, imodzi. Mafumu awa onse ndiwo makumi atatu ndi imodzi.