Yobu 38:38-40 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Pokandika pfumbi,Ndi kuundana zibuma pamodzi? Pamene ibwathama m'ngaka mwao,Nikhala mobisala kulaliramo?