Yobu 28:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Koma kuli mtapo wa siliva, Ndi malo a golidi amene amuyenga. Citsulo acitenga m'nthaka,Ndi mkuwa ausungunula kumwala