Yobu 22:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Pamenepo Elifazi wa ku Temani anayankha, nati, Kodi munthu apindulira Mulungu?Koma wanzeru angodzipindulira yekha.