Pakuti Ambuye Yehova adzandithangata Ine; cifukwa cace sindinasokonezedwa; cifukwa cace ndakhazika nkhope yanga ngati mwala, ndipo ndidziwa kuti sindidzakhala ndi manyazi.