Koma mwa Yehova yekha, wina adzati kwa Ine, muli cilungamo ndi mphamvu; ngakhale kwa Iyeyo anthu adzafika, ndi onse amene anamkwiyira, adzakhala ndi manyazi.