Sizidzaipitsa, sizidzasakaza m'phiri langa lonse loyera, cifukwa kuti dziko lapansi lidzadzala ndi odziwa Yehova, monga mdazi adzaza nyanja.