Yeremiya 16:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndiponso mau a Mulungu anadza kwa ine, kuti, Usatenge mkazi, usakhale ndi ana amuna ndi akazi m'malo muno.