Ndacokaku nyumba yanga, ndasiya colowa canga; ndapereka wokondedwa wa mtima wanga m'dzanja la adani.