Bwenzi lako wapita kuti,Mkaziwe woposa kukongola?Bwenzi lako wapambukira kuti,Tikamfunefune pamodzi nawe?