Nditawapitirira pang'ono,Ndinampeza amene moyo wanca umkonda:Ndinamgwiriziza, osamfumbatula,Mpaka nditamlowetsa m'nyumba ya amai,Ngakhale m'cipinda ca wondibala.