Popeza moto unaturuka m'Hesiboni,Cirangali ca mota m'mudzi wa Sihoni;Catha Ari wa Moabu,Eni misanje ya Arinoni.