Ndi m'masiku a Yoyakimu ansembe akulu a nyumba za makolo ndiwo: wa Seraya, Meraya; wa Yeremiya, Hananiya;