munthu wokwera pa kavalo, ndi lupanga lonyezimira, ndi mkondo wong'anipa; ndi aunyinji ophedwa, ndi cimulu ca mitembo, palibe kutha zitanda; angokhumudwa ndi zitanda;