Mbawanso inapeza nyumba,Ndi namzeze cisa cace coikamo ana ace,Pa maguwa a nsembe anu, Yehova wa makamu,Mfumu yanga ndi Mulungu wanga,