Moyo wanga ulakalaka, inde ukomokanso ndi kufuna mabwalo a Yehova;Mtima wanga ndi thupi langa zipfuulira kwa Mulungu wamoyo.