Ithe mphulupulu ya anthu oipa, ndikupemphani, koma wolungamayo mumkhazikitse:Pakuti woyesa mitima ndi imso ndiye Mulungu wolungama.