Akulu a anthu asonkhanaAkhale anthu a Mulungu wa Abrahamu:Pakuti zikopa za dziko lapansi nza Mulungu;Akwezeka kwakukuru Iyeyo.