Kodi onse ocita zopanda pace sadziwa kanthu?Pakudya anthu anga monga akudya mkate,Ndipo saitana pa Yehova.