Waucitsiru amati mumtima mwace, Kulibe Mulungu.Acita zobvunda, acita nchito zonyansa;Kulibe wakucita bwino.