1. Taonani, lemekezani Yehova, atumiki a Yehova inu nonse,Akuimirira m'nyumba ya Yehova usiku,
2. Kwezani manja anu ku malo oyera,Nimulemekeze Yehova.
3. Yehova, ali m'Ziyoni, akudalitseni;Ndiye amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 134