Monga mapiri azinga Yerusalemu,Momwemo Yehova azinga anthu ace,Kuyambira tsopano kufikira nthawi zonse.