Cifukwa ca kupasuka kwa ozunzika, cifukwa ca kuusa moyo kwa aumphawi,Ndiuka tsopano, ati Yehova; Ndidzamlonga mosungika muja alaka-lakamo.