Tipulumutseni, Yehova, Mulungu wathu,Ndi kutisokolotsa kwa amitundu,Kuti tiyamike dzina lanu loyera,Ndi kudzitamandira naco cilemekezo canu.