Masalmo 105:43-45 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Potero anaturutsa anthu ace ndi kusekerera,Osankhika ace ndi kupfuula mokondwera. Kuti asamalire malemba